None
EN
Sitima za tsopano zidzafewetsa miyoyo
['Wycliffe Njiragoma', 'Wasili Gomani', 'William Nthala', 'Isaac Chikuniwenda Mtonga']
Nation Online
Anthu okhala mozungulira, komanso pa zisumbu m’nyanja ya Malawi; pamodzi ndi ochita malonda osiyanasiyana akuyembekezera ndi chidwi kupherezera kwa lingaliro la boma lokhazikitsa sitima zinayi zatsopano pa nyanjayi. Chiyembekezochi chikudza polingalira zipsinjo zomwe zakhala zilipo kwa nthawi yaitali monga kusadalirika, komanso chiopsezo cha ngozi pa maulendo a pa nyanja zomwe sitima zatsopanozo zikuyembekezeka kudzathetsa pambali …
The post Sitima za tsopano zidzafewetsa miyoyo appeared first on Nation Online.